newsare.net
Prophet Shepherd Bushiri wati pakali pano ntchito yawo yogawa chimanga chaulere kwa a Malawi omwe akhuzidwa ndi ngozi zadzidzidzi yikupitilirabe ndipo panopa afikira anthu oposa 700 000. Mneneri wa a Bushiri a Aubrey Kusakala anena izi ku Mangochi komwe athanPakali pano tafikira anthu oposa 700 000 ndi chimanga chaulere, atero Bushiri
Prophet Shepherd Bushiri wati pakali pano ntchito yawo yogawa chimanga chaulere kwa a Malawi omwe akhuzidwa ndi ngozi zadzidzidzi yikupitilirabe ndipo panopa afikira anthu oposa 700 000. Mneneri wa a Bushiri a Aubrey Kusakala anena izi ku Mangochi komwe athandiza mabanja oposa 200 mdera la Senior Chief Nankumba ku Monkey-Bay m’boma la Mangochi. A Bushiri […] The post Pakali pano tafikira anthu oposa 700 000 ndi chimanga chaulere, atero Bushiri appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more