newsare.net
Alimi a fodya omwe anagulitsa fodya wao sabata loyamba la msika wafodya adandaula kuti sanalandirebe ndalama zawo pomwe msika walowa sabata yachiwiri. Mmodzi mwa alimiwa a Msaiwale Zakaliya omwe analinso ndi anzawo ena oposa khumi aku Chamama m’boma laAlimi a fodya adandaula ati sakulandirabe ndalama zawo ngakhale anagulisa fodya kalekale
Alimi a fodya omwe anagulitsa fodya wao sabata loyamba la msika wafodya adandaula kuti sanalandirebe ndalama zawo pomwe msika walowa sabata yachiwiri. Mmodzi mwa alimiwa a Msaiwale Zakaliya omwe analinso ndi anzawo ena oposa khumi aku Chamama m’boma la Kasungu ati ali kakasi chifukwa adatumiza msanga fodya kuti atumize ana ku sukulu. Iwo ati malamulo […] The post Alimi a fodya adandaula ati sakulandirabe ndalama zawo ngakhale anagulisa fodya kalekale appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more