newsare.net
Bwalo lalikulu la milandu ku Lilongwe lathetsa umodzi mwa milandu yomwe mkulu wakale wa banki ya Reserve a Dalitso Kabambe ndi wachiwiri wao a Henry Mathanga akhala akuyankha okhudza kuganiziridwa kuti ankanamiza bungwe lopereka ngongole la International MoneKhoti lichosa mulandu umodzi pa milandu iwiri yomwe akuzenga a Dalitso Kabambe: Akuti boma lilibe umboni
Bwalo lalikulu la milandu ku Lilongwe lathetsa umodzi mwa milandu yomwe mkulu wakale wa banki ya Reserve a Dalitso Kabambe ndi wachiwiri wao a Henry Mathanga akhala akuyankha okhudza kuganiziridwa kuti ankanamiza bungwe lopereka ngongole la International Monetary Fund. Malingana ndi chigamulo chomwe apereka oweruza a Redson Kapindu, mulandu omwe wathetsedwa ndi oti awiriwa anagwiritsa […] The post Khoti lichosa mulandu umodzi pa milandu iwiri yomwe akuzenga a Dalitso Kabambe: Akuti boma lilibe umboni appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi. Read more